Skip to content
The Believer's Library

Biblica® Open Godʼs Word in Contemporary Chichewa

Psalms 131 OCCL

Side by side with the Father's Heart Bible™

Nyimbo yoyimba pokwera ku Yerusalemu. Salimo la Davide.

1Inu Yehova, mtima wanga siwodzikuza,maso anga siwonyada;sinditengeteka mtimandi zinthu zapamwamba ndi zodabwitsa.

2Koma moyo wanga ndawutontholetsandi kuwukhalitsa chete ngati mwana amene amayi ake amuletsa kuyamwa,moyo wanga mʼkati mwanga uli ngati mwana amene amuletsa kuyamwa.

3Yembekeza Yehova, iwe Israeli,kuyambira tsopano mpaka muyaya.

Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero™ Mwini © 2002, 2016 ndi Biblica, Inc. Biblica® Open Godʼs Word in Contemporary Chichewa™ Copyright © 2002, 2016 by Biblica, Inc. “Biblica” ndilo dzina lodziwika la ntchitoyi ku United States limene linalembetsedwa ndi Biblica mwini. Limagwiritsidwa ntchito ndi chilolezo. “Biblica” is a trademark registered in the United States Patent and Trademark Office by Biblica, Inc. Used with permission.
Biblica® Open Godʼs Word in Contemporary Chichewa · Creative Commons - Attribution-ShareAlike [CC BY-SA]