Skip to content
The Believer's Library

Biblica® Open Godʼs Word in Contemporary Chichewa

1 Chronicles 25 OCCL

Show OCCL only
Verse × ×
1 David and the army commanders set apart some of the sons of Asaph, Heman, and Jeduthun for service, who prophesied with lyres, harps, and cymbals. Their numbers, by task, were: Davide ndi atsogoleri a asilikali anapatula ena mwa ana a Asafu, Hemani ndi Yedutuni ku utumiki wa uneneri pogwiritsa ntchito apangwe, azeze ndi ziwaya zamalipenga. Tsopano nawu mndandanda wa anthu amene ankagwira ntchito imeneyi:
2 Sons of Asaph: Zaccur, Joseph, Nethaniah, Asharelah, the sons of Asaph—under Asaph's direction, prophesying under the king's direction. Kuchokera kwa ana a Asafu: Zakuri, Yosefe, Netaniya ndi Asareli. Ana a Asafu amalamulidwa ndi Asafu ndipo amanenera moyangʼaniridwa ndi mfumu.
3 Jeduthun's sons: Gedaliah, Zeri, Jeshaiah, Shimei, Hashabiah, Mattithiah—six, guided by their father Jeduthun, prophesied with the lyre, thanking and praising our Father. Kwa Yedutuni, kuchokera kwa ana ake: Gedaliya, Zeri, Yesaya, Simei, Hasabiya ndi Matitiya. Onse analipo 9 ndipo amayangʼaniridwa ndi Yedutuni abambo awo, amene amanenera pogwiritsa ntchito apangwe poyamika ndi kutamanda Yehova.
4 Of Heman, sons of Heman: Bukkiah, Mattaniah, Uzziel, Shebuel, Jerimoth, Hananiah, Hanani, Eliathah, Giddalti, Romamti-ezer, Joshbekashah, Mallothi, Hothir, Mahazioth. Kwa Hemani, kuchokera kwa ana ake: Bukiya, Mataniya, Uzieli, Subaeli ndi Yerimoti; Hananiya, Hanani, Eliata, Gidaliti ndi Romamiti-Ezeri; Yosibakasa, Maloti, Hotiri ndi Mahazioti.
5 All these were sons of Heman, the king's seer, given through our Father's word to lift Heman up. Our Father gave Heman fourteen sons and three daughters. Onsewa anali ana a Hemani mlosi wa mfumu. Iye anapatsidwa anawa potsata mawu a Mulungu akuti adzamukweza. Mulungu anapatsa Hemani ana aamuna 14 ndi ana aakazi atatu.
6 All these were under their father's direction for song in the house of our Father, with cymbals, harps, and lyres for the service of the house of our Father; Asaph, Jeduthun, and Heman were under the king's direction. Anthu onsewa ankayangʼaniridwa ndi makolo awo pa mayimbidwe a mʼNyumba ya Yehova. Iwowatu ankayimba ndi ziwaya zamalipenga, azeze ndi apangwe potumikira mʼNyumba ya Mulungu. Koma Asafu, Yedutuni ndi Hemani amayangʼaniridwa ndi mfumu.
7 Their number, with their kin trained to sing to our Father—all skilled—was 288. Iwo pamodzi ndi abale awo onse ophunzitsidwa ndi aluso loyimbira Yehova chiwerengero chawo chinali 288.
8 And they cast lots for their duties, small and great alike, teacher and pupil alike. Angʼonoangʼono ndi akulu omwe, mphunzitsi ndi wophunzira yemwe anachita maere pa ntchito zawo.
9 The first lot came out for Asaph, to Joseph; the second, Gedaliah with his brothers and sons, twelve. Maere woyamba amene anali a Asafu, anagwera Yosefe, ana ndi abale ake. 12 Maere achiwiri anagwera Gedaliya, ndi abale ake ndi ana ake. 12
10 The third to Zaccur, his sons and his brothers, twelve; Maere achitatu anagwera Zakuri, ana ake ndi abale ake. 12
11 the fourth to Izri, his sons and his brothers, twelve; Maere achinayi anagwera Iziri, ana ake ndi abale ake. 12
12 the fifth to Nethaniah, his sons and his brothers, twelve; Maere achisanu anagwera Netaniya, ana ake ndi abale ake. 12
13 the sixth to Bukkiah, his sons and his brothers, twelve; Maere achisanu ndi chimodzi anagwera Bukiya, ana ake ndi abale ake. 12
14 the seventh to Jesarelah, his sons and his brothers, twelve; Maere achisanu ndi chiwiri anagwera Yesarela, ana ake ndi abale ake. 12
15 the eighth to Jeshaiah, his sons and his brothers, twelve; Maere achisanu ndi chitatu anagwera Yeshaya, ana ake ndi abale ake. 12
16 the ninth to Mattaniah, his sons and his brothers, twelve; Maere achisanu ndi chinayi anagwera Mataniya, ana ake ndi abale ake. 12
17 the tenth to Shimei, his sons and his brothers, twelve; Maere a khumi anagwera Simei, ana ake ndi abale ake. 12
18 the eleventh to Azarel, his sons and his brothers, twelve; Maere a 11 anagwera Azareli, ana ake ndi abale ake. 12
19 the twelfth to Hashabiah, his sons and his brothers, twelve; Maere a 12 anagwera Hasabiya, ana ake ndi abale ake. 12
20 the thirteenth to Shubael, his sons and his brothers, twelve; Maere a 13 anagwera Subaeli, ana ake ndi abale ake. 12
21 the fourteenth to Mattithiah, his sons and his brothers, twelve; Maere a 14 anagwera Matitiya, ana ake ndi abale ake. 12
22 the fifteenth to Jeremoth, his sons and his brothers, twelve; Maere a 15 anagwera Yeremoti, ana ake ndi abale ake. 12
23 the sixteenth to Hananiah, his sons and his brothers, twelve; Maere a 16 anagwera Hananiya, ana ake ndi abale ake. 12
24 the seventeenth to Joshbekashah, his sons and his brothers, twelve; Maere a 17 anagwera Yosibakasa, ana ake ndi abale ake. 12
25 the eighteenth to Hanani, his sons and his brothers, twelve; Maere a 18 anagwera Hanani, ana ake ndi abale ake. 12
26 the nineteenth to Mallothi, his sons and his brothers, twelve; Maere a 19 anagwera Maloti, ana ake ndi abale ake. 12
27 the twentieth to Eliathah, his sons and his brothers, twelve; Maere a 20 anagwera Eliyata, ana ake ndi abale ake. 12
28 the twenty-first to Hothir, his sons and his brothers, twelve; Maere a 21 anagwera Hotiri, ana ake ndi abale ake. 12
29 the twenty-second to Giddalti, his sons and his brothers, twelve; Maere a 22 anagwera Gidaliti, ana ake ndi abale ake. 12
30 the twenty-third to Mahazioth, his sons and his brothers, twelve; Maere a 23 anagwera Mahazioti, ana ake ndi abale ake. 12
31 the twenty-fourth to Romamti-ezer, his sons and his brothers, twelve. Maere a 24 anagwera Romamiti-Ezeri, ana ake ndi abale ake 12.
FHB

Scripture from Father’s Heart Bible™. © 2026 Spirit Media Publishing, the imprint of Spirit Media Inc. All rights reserved. In Divine Voice™ Color, the words spoken by our Father show in blue, the words of the Son in red, and the words of the Spirit in purple.

OCCL

Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero™ Mwini © 2002, 2016 ndi Biblica, Inc. Biblica® Open Godʼs Word in Contemporary Chichewa™ Copyright © 2002, 2016 by Biblica, Inc. “Biblica” ndilo dzina lodziwika la ntchitoyi ku United States limene linalembetsedwa ndi Biblica mwini. Limagwiritsidwa ntchito ndi chilolezo. “Biblica” is a trademark registered in the United States Patent and Trademark Office by Biblica, Inc. Used with permission.
Biblica® Open Godʼs Word in Contemporary Chichewa · Creative Commons - Attribution-ShareAlike [CC BY-SA]